Proverbs 24:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usamanena kuti, “Ndidzamchitira monga momwe iye wandichitira ine, ndidzamlipsira chifukwa cha zomwe iye wandichitira ine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usanene, Ndidzamchitira zomwezo anandichitira ine ndidzabwereza munthuyo monga mwa machitidwe ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Usanene kuti, “Ine ndidzamuchitira iye monga momwe wandichitira ine; ndidzamubwezera munthu ameneyo zimene anandichitira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usanene, Ndidzamcitira zomwezo anandicitira ine; Ndidzabwereza munthuyo monga mwa macitidwe ace.