Proverbs 24:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkayenda m'mbali mwa munda wa munthu waulesi, m'mbali mwa munda wamphesa wa munthu wopanda nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinapita pa munda wa waulesi, polima mphesa munthu wosowa nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinkayenda mʼmbali mwa munda wa munthu waulesi ndinadutsa munda wamphesa wa munthu wopanda nzeru.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinapita pa munda wa wolesi, Polima mphesa munthu wosowa nzeru.