Proverbs 24:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'minda monsemo munali mutamera minga yokhayokha, m'nthaka imeneyo munali mutamera khwisa, ndipo mpanda wake wamiyala unali utagwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ponsepo panamera minga, ndi kuwirirapo khwisa; tchinga lake lamiyala ndi kupasuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndinapeza kuti paliponse mʼmundamo munali mutamera minga, mʼnthaka imeneyo munali mutamera khwisa, ndipo mpanda wake wamiyala unali utawonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ponsepo panamera minga, Ndi kuwirirapo khwisa; Chinga lace lamiyala ndi kupasuka.