Proverbs 24:34 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
umphaŵi udzakufikira monga mbala, kusauka kudzakupeza ngati mbala yachifwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala; ndi kusauka kwako ngati munthu wachikopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
umphawi udzafika pa iwe ngati mbala ndipo usiwa udzakupeza ngati munthu wachifwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo umphawi wako udzafika ngati mbala; Ndi kusauka kwako ngati munthu wacikopa.