Proverbs 24:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wanzeru ndi wamphamvu kupambana munthu wa nyonga zambiri, munthu wophunzira amaposa munthu wamphamvu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamuna wanzeru ngwamphamvu; munthu wodziwa ankabe nalimba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wodziwa zinthu ali ndi mphamvu yayikulu kuposa munthu wanyonga zambiri, ndipo munthu wachidziwitso amaposa munthu wamphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamuna wanzeru ngwamphamvu; Munthu wodziwa ankabe nalimba.