Proverbs 27:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwana wanga, ukhale ndi nzeru, ukondwetse mtima wanga, kuti choncho ndithe kumuyankha amene amandinyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwananga, khala wanzeru, nukondweretse mtima wanga; kuti ndimuyankhe yemwe anditonza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wanga, khala wanzeru, ndipo ukondweretse mtima wanga; pamenepo ine ndidzatha kuyankha aliyense amene amandinyoza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwananga, khala wanzeru, nukondweretse mtima wanga; Kuti ndimuyankhe yemwe anditonza.