Proverbs 27:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wochenjera akaona choopsa amabisala, koma wopusa amangopitirira ndipo amanong'oneza bondo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wochenjera aona zoipa, nabisala; koma achibwana angopitirira, nalipitsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wochenjera akaona choopsa amabisala, koma munthu wopusa amangopitirira ndipo amakumana ndi mavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wocenjera aona zoipa, nabisala; Koma acibwana angopitirira, nalipitsidwa.