Proverbs 27:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wopatsa mnzake moni mofuula m'mamaŵa kwambiri, adzamuyesa kuti akutemberera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yemwe adalitsa mnzake ndi mau akulu pouka mamawa, anthu adzachiyesa chimenecho temberero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu apatsa mnzake moni mofuwula mmamawa kwambiri, anthu adzamuyesa kuti akutemberera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yemwe adalitsa mnzace ndi mau akuru pouka mamawa, Anthu adzaciyesa cimeneco temberero.