Proverbs 27:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chitsiru ngakhale uchisinje mu mtondo ndi munsi pamodzi ndi chimanga, kupusa kwake sikudzachoka konse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ungakhale ukonola chitsiru m'mtondo ndi munsi, pamodzi ndi mphale, koma utsiru wake sudzamchoka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale utakonola chitsiru mu mtondo ndi musi ngati chimanga, uchitsiru wakewo sudzachoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ungakhaleukonolacitsirum'mtondo ndi munsi, pamodzi ndi mphale, Koma utsiru wace sudzamcoka.