Proverbs 27:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwala ndi wolemera, ndipo mchenganso ndi wolemera kwambiri, koma makani a chitsiru ndi oposa zonsezo kulemera kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwala ulemera, mchenga ndiwo katundu; koma mkwiyo wa chitsiru upambana kulemera kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwala ndi wolemera ndipo mchenganso ndi wolemera kwambiri, koma makani a chitsiru ndi oposa zonsezo kulemera kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwala ulemera, mcenga ndiwo katundu; Koma mkwiyo wa citsiru upambana kulemera kwace.