Proverbs 27:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwiyo umadzetsa nkhanza, kupsa mtima kumachititsa zoopsa, koma nsanje imabweretsa zoipa zopambana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kupweteka mtima nkwa nkhanza, mkwiyo usefuka; koma ndani angalakike ndi nsanje?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mkwiyo umadzetsa nkhanza ndipo kupsa mtima kumachititsa zoopsa. Koma nsanje imachita zoopsa zopambana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kupweteka mtima nkwa nkhanza, mkwiyo usefuka; Koma ndani angalakike ndi nsanje?