Proverbs 27:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mafuta ndi zonunkhira zimasangalatsa mtima, koma kukoma kwa bwenzi kwagona pa malangizo ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mafuta ndi zonunkhira zikondweretsa mtima, ndi ubwino wa bwenzi uteronso pakupangira uphungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mafuta ndi zonunkhira zimasangalatsa mtima, ndipo kukoma mtima kwa bwenzi kwagona pa malangizo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mafuta ndi zonunkhira zikondweretsa mtima, Ndi ubwino wa bwenzi uteronso pakupangira uphungu,