Proverbs 28:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu abwino akapambana, pamakhala chikondwerero chachikulu, koma oipa mtima akalandira ulamuliro, anthu amabisala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Posekera olungama pali ulemerero wambiri; koma pouka oipa anthu amabisala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene olungama apambana pamakhala chikondwerero chachikulu; koma pamene anthu oyipa apatsidwa ulamuliro, anthu amabisala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Posekera olungama pali ulemerero wambiri; Koma pouka oipa anthu amabisala.