Proverbs 28:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wobisa machimo ake sadzaona mwai, koma woulula ndi kuleka machimo, adzalandira chifundo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobisa machimo ake sadzaona mwai; koma wakuwavomereza, nawasiya adzachitidwa chifundo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wobisa machimo ake sadzaona mwayi, koma aliyense amene awulula ndi kuleka machimowo, adzalandira chifundo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobisa macimo ace sadzaona mwai; Koma wakuwabvomereza, nawasiya adzacitidwa cifundo.