Proverbs 28:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi wodala munthu amene amaopa Chauta nthaŵi zonse, koma woumitsa mtima wake adzagwa m'tsoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wodala munthu wakuopa kosalekeza; koma woumitsa mtima wake adzagwa m'zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi wodala munthu amene amaopa Yehova nthawi zonse, koma amene aumitsa mtima wake adzagwa mʼmavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wodala munthu wakuopakosalekeza; Koma woumitsa mtima wace adzagwa m'zoipa.