Proverbs 28:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga muja umakhalira mkango wobangula kapena chimbalangondo cholusa, ndimonso imakhalira mfumu yoipa mtima kwa anthu osauka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga mkango wobangula ndi chilombo choyendayenda, momwemo mfumu yoipa ya anthu osauka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mkango wobuma kapena chimbalangondo cholusa ndi mmenenso amakhalira munthu woyipa akamalamulira anthu osauka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga mkango wobangula ndi cirombo coyendayenda, Momwemo mfumu yoipa ya anthu osauka.