Proverbs 28:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wolamulira amene samvetsa zinthu amapondereza anthu mwankhanza, koma wodana ndi phindu loipa amatalikitsa masiku ake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kalonga wosowa nzeru apambana kusautsa; koma yemwe ada chisiriro adzatanimphitsa moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wolamulira amene samvetsa zinthu ndiye amakhala wankhanza koma amene amadana ndi phindu lopeza mwachinyengo adzakhala ndi moyo wautali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kalonga wosowa nzeru apambana kusautsa; Koma yemwe ada cisiriro adzatanimphitsa moyo wace.