Proverbs 28:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wolima m'munda mwake adzakhala ndi chakudya chambiri, koma wonka nafuna zopanda pake adzasauka kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolima munda wake zakudya zidzamkwanira; koma wotsata anthu opanda pake umphawi udzamkwanira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amalima mʼmunda mwake adzakhala ndi chakudya chochuluka, koma amene amangosewera adzakhala mʼmphawi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolima munda wace zakudya zidzamkwanira; Koma wotsata anthu opanda pace umphawi udzamkwanira.