Proverbs 28:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wokhulupirika adzakhala ndi madalitso ambiri, koma wofunitsitsa kulemera msanga sadzalephera kupeza chilango.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu wokhulupirika ali ndi madalitso ambiri; koma wokangaza kulemera sadzapulumuka chilango.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wokhulupirika adzadalitsika kwambiri, koma wofuna kulemera mofulumira adzalangidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu wokhulupirika ali ndi madalitso ambiri; Koma wokangaza kulemera sadzapulumuka cilango,