Proverbs 28:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wakaliwumira amafunitsitsa kulemera mofulumira, koma sadziŵa kuti umphaŵi udzamgwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwini diso lankhwenzule akangaza kulemera, osadziwa kuti umphawi udzamfikira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wowumira amafunitsitsa kulemera koma sazindikira kuti umphawi udzamugwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwini diso lankhwenzule akangaza kulemera, Osadziwa kuti umphawi udzamfikira.