Proverbs 28:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wobera atate ake kapena amai ake namanena kuti kutero sikulakwa, ameneyo ndi mnzake wa munthu woononga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wobera atate wake, pena amake, nati, Palibe kulakwa; ndiye mnzake wa munthu wopasula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amabera abambo ake kapena amayi ake namanena kuti “kumeneko sikulakwa,” ndi mnzake wa munthu amene amasakaza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wobera atate wace, pena amace, nati, Palibe kulakwa; Ndiye mnzace wa munthu wopasula.