Proverbs 28:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa samvetsa kuti chilungamo nchiyani, koma amene amatsata kufuna kwa Chauta amachimvetsa kwathunthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oipa samvetsetsa chiweruzo; koma omwe afuna Yehova amvetsetsa zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu oyipa samvetsa za chiweruzo cholungama, koma amene amafuna kuchita zimene Yehova afuna amachimvetsetsa bwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oipa samvetsetsa ciweruzo; Koma omwe afuna Yehova amvetsetsa zonse.