Proverbs 28:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amatsata malamulo ndiye mwana wanzeru, koma amene amayenda ndi anthu adyera, amachititsa atate ake manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wosunga chilamulo ndiye mwana wozindikira; koma mnzao wa adyera achititsa atate wake manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene amasunga malamulo ndi mwana wozindikira zinthu, koma amene amayenda ndi anthu adyera amachititsa manyazi abambo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wosunga cilamulo ndiye mwana wozindikira; Koma mnzao wa adyera acititsa atate wace manyazi.