Proverbs 29:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu okhetsa magazi amadana ndi munthu wosalakwa, koma anthu angwiro amateteza moyo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu ankhanza ada wangwiro; koma oongoka mtima asamalira moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu okhetsa magazi amadana ndi munthu wangwiro koma anthu olungama amasamalira moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu ankhanza ada wangwiro; Koma oongoka mtima asamalira moyowace.