Proverbs 29:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mkwapulo ndi chidzudzulo zimapatsa nzeru, koma mwana womamlekerera amachititsa amake manyazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nthyole ndi chidzudzulo zipatsa nzeru; koma mwana womlekerera achititsa amake manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndodo ndi chidzudzulo zimapatsa nzeru koma mwana womulekerera amachititsa amayi ake manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ntyole ndi cidzudzulo zipatsa nzeru; Koma mwana womlekerera acititsa amace manyazi.