Proverbs 29:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Oipa akamalamulira, zolakwa zimachuluka, koma ochita chilungamo adzaona kugwa kwa oipawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pochuluka oipa zolakwa zichuluka; koma olungama adzaona kugwa kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oyipa akamalamulira zoyipa zimachuluka, koma anthu olungama adzaona kugwa kwa anthu oyipawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pocuruka oipa zolakwa zicuruka; Koma olungama adzaona kugwa kwao.