Proverbs 29:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uzimlanga mwana wako ndipo adzakupatsa mtendere mu mtima, adzakondweretsa mtima wako m'tsogolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Langiza mwana wako, ndipo adzakupumitsa; nadzasangalatsa moyo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umulange mwana wako ndipo adzakupatsa mtendere ndi kusangalatsa mtima wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Langiza mwana wako, ndipo adzakupumitsa; Nadzasangalatsa moyo wako.