Proverbs 29:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kumene kulibe mithenga yochokera kwa Mulungu, anthu saweruzika, ndi wodala munthu amene amatsata malamulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popanda chivumbulutso anthu amasauka; koma wosunga chilamulo adalitsika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati uthenga wochokera kwa Yehova supezeka anthu amangochita zofuna zawo; koma wodala ndi amene amasunga malamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popanda cibvumbulutso anthu amasauka; Koma wosunga cilamulo adalitsika.