Proverbs 29:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mu dziko mukakhala chilungamo, anthu amakondwa, koma chilungamo chikasoŵa, anthu amadandaula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pochuluka olungama anthu akondwa; koma polamulira woipa anthu ausa moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama akamalamulira mʼdziko anthu amakondwa, koma ngati dziko lilamulidwa ndi anthu oyipa mtima anthu amadandaula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pocuruka olungama anthu akondwa; Koma polamulira woipa anthu ausa moyo.