Proverbs 29:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale chitsiru chomwe nkuti ndiponi pali chikhulupiriro, koma osati munthu wodziyesa wanzeru pamene ali wopusa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi uona munthu wansontho m'mau ake? Ngakhale chitsiru chidzachenjera, koma ameneyo ai.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale munthu wa uchitsiru nʼkuti ndiponi popeza chikhulupiriro chilipo kuposa munthu wodziyesa yekha kuti ndi wanzeru poyankhula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi uona munthu wansontho m'mau ace? Ngakhale citsiru cidzacenjera, koma ameneyo ai.