Proverbs 29:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amene amasasatitsa kapolo wake kuyambira ali mwana, pomaliza pake adzapeza kuti kapoloyo wasanduka mloŵachuma wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yemwe alera kapolo wake mwa ufulu kuyambira ubwana wake, pambuyo pake adzadziyesa mwana wobala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati munthu asasatitsa wantchito wake kuyambira ali mwana, potsirizira adzapeza kuti wantchitoyo wasanduka mlowachuma wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yemwe alera kapolo wace mwa ufulu kuyambira ubwana wace, Pambuyo pace adzadziyesa mwana wobala.