Proverbs 29:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wamangaŵa amautsa mikangano, munthu wokalipakalipa amabweretsa zolakwa zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamuna wamkwiyo aputa makangano; waukali achuluka zolakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wamkwiyo amayambitsa mikangano, ndipo munthu waukali amachita zolakwa zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamuna wamkwiyo aputa makangano; Waukali acuruka zolakwa.