Proverbs 29:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuwopa anthu kuli ngati msampha, koma wodalira Chauta amakhala pabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuopa anthu kutchera msampha; koma wokhulupirira Yehova adzapulumuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuopa munthu kudzakhala ngati msampha, koma aliyense amene amadalira Yehova adzatetezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuopa anthu kuchera msampha; Koma wokhulupirira Yehova adzapulumuka,