Proverbs 29:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu osoŵa chilungamo amanyansa anthu ochita chilungamo, monga momwe anthu abwino amanyansira anthu oipa mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu woipa anyansa olungama; ndipo woongoka m'njira anyansa wochimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu olungama amanyansidwa ndi anthu achinyengo; koma anthu oyipa amanyansidwa ndi anthu a mtima wowongoka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu woipa anyansa olungama; Ndipo woongoka m'njira anyansa wocimwa.