Proverbs 29:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mfumu imalimbitsa dziko pakuweruza molungama, koma imene imaumiriza anthu kuti aipatse ziphuphu, imaononga dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu akhazikitsa dziko ndi chiweruzo; koma wosonkhetsa anthu mphatso alipululutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mfumu imalimbitsa dziko poweruza mwachilungamo, koma mfumu imene imawumiriza anthu kuti ayipatse mphatso imawononga dziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu akhazikitsa dziko ndi ciweruzo; Koma wosonkhetsa anthu mphatso alipululutsa.