Proverbs 29:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu woipa amakodwa ndi zolakwa zake, koma wochita chilungamo amakhala wokondwa ndi womasuka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kulakwa kwa woipa muli msampha; koma wolungama aimba, nakondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu woyipa amakodwa ndi machimo ake, koma wochita chilungamo amayimba lokoma.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kulakwa kwa woipa muli msampha; Koma wolungama ayimba, nakondwera.