Proverbs 29:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu wokoma mtima amasamalira zoyenerera osauka, koma munthu woipa salabadako za zimenezo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama asamalira mlandu wa osauka; koma woipa alibe nzeru yakuudziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu wolungama amasamalira anthu osauka, koma woyipa salabadira zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama asamalira mlandu wa osauka; Koma woipa alibe nzeru yakuudziwa.