Proverbs 29:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu onyoza akhoza kuyatsa mzinda, koma anthu anzeru amabweza ukali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu onyoza atentha mudzi; koma anzeru alezetsa mkwiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onyoza atha kuwutsa ziwawa mu mzinda, koma anthu anzeru amaletsa ukali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu onyoza atentha mudzi; Koma anzeru alezetsa mkwiyo.