Proverbs 30:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa mau a Aguri, mwana wa Yake, wa ku Masa: Inu Mulungu, ine ndatopa. Inu Mulungu, ine ndatopa, ndalefukiratu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a Aguri mwana wa Yake; uthenga. Munthuyo anati, Ndadzitopetsa, Mulungu; ndadzitopetsa, Mulungu, ndathedwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nawa mawu a Aguri mwana wa Yake wa ku Masa: Munthuyo anati kwa Itieli, “Inu Mulungu, ine ndatopa. Inu Mulungu, ine ndatopa. Ndalefukiratu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a Aguri mwana wa Yake; uthenga. Munthuyo anati, Ndadzitopetsa, Mulungu; Ndadzitopetsa, Mulungu, ndathedwa;