Proverbs 30:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pali zinthu zitatu zimene zimandidabwitsa kwambiri. Pali zinthu zinai zimene sindizimvetsa konse, zinthuzo ndi izi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zinthu zitatu zindithetsa nzeru, ngakhale zinai, sindizidziwa:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali zinthu zitatu zimene zimandidabwitsa, zinthu zinayi zimene ine sindizimvetsetsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zinthu zitatu zindithetsa nzeru, Ngakhale zinai, sindizidziwa: