Proverbs 30:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mene umaulukira mphamba mu mlengalenga, m'mene imayendera njoka pa thanthwe, m'mene chimayendera chombo pa nyanja yakuya, ndiponso m'mene mwamuna amachitira akakhala ndi namwali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Njira ya mphungu m'mlengalenga, njira ya njoka pamwala, njira ya ngalawa pakati pa nyanja, njira ya mwamuna ndi namwali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ndi izi: mmene chiwulukira chiwombankhanga mlengalenga; mmene iyendera njoka pa thanthwe; mmene chiyendera chombo pa nyanja; ndiponso mmene mwamuna achitira akakhala ndi namwali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Njira ya mphungu m'mlengalenga, Njira ya njoka pamwala, Njira ya ngalawa pakati pa nyanja. Njira ya mwamuna ndi namwali.