Proverbs 30:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mene amachitira mkazi akachita chigololo amatere: amati akadya nkupukuta pakamwa, namanena kuti, “Palibe chimene ndalakwa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chomwecho njira ya mkazi wachigololo; adya, napukuta pakamwa, nati, Sindinachita zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Umu ndi mʼmene mkazi amachitira atachita chigololo: Atatha kudya ndi kupukuta pakamwa pake iye amanena kuti “Sindinachite kalikonse kolakwa.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Comweco njira ya mkazi wacigololo; Adya, napukuta pakamwa, nati, Sindinacita zoipa,