Proverbs 30:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pali zinthu zitatu zimene dziko lapansi limanjenjemera nazo. Pali zinthu zinai zimene dziko lapansi silingathe kuzipirira:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha zinthu zitatu dziko linthunthumira; ngakhale chifukwa cha zinai silingathe kupirira nazo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali zinthu zitatu zimene zimanjenjemeretsa dziko lapansi, pali zinthu zinayi zimene dziko lapansi silingathe kuzipirira:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca zinthu zitatu dziko linthunthumira; Ngakhale cifukwa ca zinai silingathe kupirira nazo: