Proverbs 30:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kapolo akasanduka mfumu, chitsiru chikakhuta,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa cha kapolo pamene ali mfumu; ndi chitsiru chitakhuta zakudya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kapolo amene wasanduka mfumu, chitsiru chimene chakhuta,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca kapolo pamene ali mfumu; Ndi citsiru citakhuta zakudya;