Proverbs 30:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mkazi wonyozeka akakwatiwa, ndiponso mdzakazi akalanda malo a mbuyake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa cha mkazi wodedwa wokwatidwa; ndi mdzakazi amene adzalandira cholowa cha mbuyake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mkazi wonyozeka akakwatiwa ndiponso wantchito wamkazi akalanda mwamuna wa mbuye wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca mkazi wodedwa wokwatidwa; Ndi mdzakazi amene adzalandira colowa ca mbuyace.