Proverbs 30:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pali zinthu zinai zing'onozing'ono pa dziko lapansi, koma ndi zochenjera kwambiri:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zilipo zinai zili zazing'ono padziko; koma zipambana kukhala zanzeru:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali zinthu zinayi zingʼonozingʼono pa dziko lapansi, komatu ndi zochenjera kwambiri:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ziripo zinai ziri zazing'ono padziko; Koma zipambana kukhala zanzeru: