Proverbs 30:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nyerere zili ngati anthu opanda nyonga, komabe zimakonzeratu chakudya chake m'chilimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nyerere ndi mtundu wosalimba, koma zitengeratu zakudya zao m'malimwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nyerere zili ngati anthu opanda mphamvu, komatu zimasungiratu chakudya chake nthawi ya chilimwe;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nyerere ndi mtundu wosalimba, Koma zitengeratu zakudya zao m'malimwe.