Proverbs 30:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbira zili ngati anthu opanda nyonga, komabe zimakonza pokhala pake m'matanthwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbira ndi mtundu wopanda mphamvu, koma ziika nyumba zao m'matanthwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mbira zili ngati anthu opanda mphamvu komatu zimakonza pokhalapo pawo mʼmiyala;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbira ndi mtundu wopanda mphamvu, Koma ziika nyumba zao m'matanthwe.