Proverbs 30:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Buluzi ungathe kumugwira ndi manja, komabe amakhala m'nyumba za mafumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Buluzi ungamgwire m'manja, koma ali m'nyumba za mafumu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Buluzi ungathe kumugwira mʼmanja komatu amapezeka mʼnyumba za mafumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Buluzi ungamgwire m'manja, Koma ali m'nyumba za mafumu.