Proverbs 30:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalole kuti ndikhale wabodza kapena wonama. Ndisakhale mmphaŵi kapena khumutcha. Muzindidyetsa chakudya chondiyenera,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundichotsere kutali zachabe ndi mabodza; musandipatse umphawi, ngakhale chuma, mundidyetse zakudya zondiyenera;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choyamba, mundichotsere kutali nane mabodza ndi chinyengo. Chachiwiri, ndisakhale mʼmphawi kapena munthu wachuma. Koma muzindidyetsa chakudya chondikwanira tsiku ndi tsiku
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundicotsere kutari zacabe ndi mabodza; Musandipatse umphawi, ngakhale cuma, Mundidyetse zakudya zondiyenera;